Lyrical Monday: Tiri Ndi Mphamvu (We’ve Got The Power)

Chichewa:

Tigwirane manja, tigwirizane

Adani athu onse adzagwa pamapazi athu

Chomwe timange padziko

Chidzamangidwa kumwamba

Mu Dzina la Yesu satana adzathawa


Chorus:

Poti tiri ndi mphamvu mu Dzina la Yesu

Ee tiri ndi mphamvu mu dzina la Ambuye

Ngakhale satana akwiye

Sitingagonjetsedwebe

Poti tiri ndi mphamvu mu Dzina la Ambuye


Kwa zaka zambirino, satana wati atilepheletse

Koma Mkwatibwi wa Yesu, Mbuye ali ndi moyobe

Monga asirikali amphamvu, tingoguba cha mtsogolo

Kugonjetsa nkhondo zonse

Poti Ambuye ali mbali yathu!


English:

Give me your hand, let’s agree together

Then all of our enemies will crumble at our feet

For whatever we bind on earth

Shall be bound in Heaven

At the Name of Jesus, satan has to flee


Chorus:

‘Cause we’ve got the power in the Name of Jesus

Yes we’ve got the power in the Name of the Lord

Though satan rages we cannot be defeated

‘Cause we’ve got the power in the Name of the Lord


For many years now satan has tried to stop us

But the Bride of Jesus, Lord, we’re still alive

Like a mighty Army we’ll keep marching onward

Winning every battle, ‘cause the Lord’s on our side!


This is the Chichewa version


May you have a blessed week!


Cheers!

2 comments:

Rising Up From My Brokenness

I was broken. For about three whole years. I was deeply disappointed with life. "The future" turned out to be much different than ...